Baibulo

Baibulo ndi buku lopatulika lomwe limakhulupiliwa kuti linapatsidwa kwa anthu kuchokera kwa Mulungu.

Ilo lagawidwa muzigawo ziwiri- malemba a Chiheberi ndi malemba a Chigriki. Mabukhu amene amagwiritsidwa ntchito ku Chiyuda amatchedwa Tanaka kapena Baibulo la Chiyunda. Mabukhu amene amagwiritsidwa ntchito mu Chikhristu amatcheda Bukhu Loyera, Mau a Mulungu kapena Baibulo la chi Khristu. Chikhristu chimatenga ma bukhu ena a Baibulo la Chiyuda ku Chipangano cha kale, ngakhale ma bukhu awa amasiyana pa dongosolo lake ndipo ma baibulo ena ali ndi mabukhu owonjezera. baibulo la Chikhristu lili ndi mbali ina ya chiwiri yotchedwa Chipangano cha Tsopano.

Baibulo
Baibulo

Mabukhu a Baibulo

Ma bukhu a baibulo amayalidwa mofanana mu zitanthauziro zosiyana siyana. Baibulo la Chikhristu linagawidwa mbali ziwili: Chipangano cha Kale ndi Chipangano cha Tsopano.

Chipangano cha Kale

Genesis

Ekesodo

20

Numeri

Deuteronomo

Yoswa

Oweruza

Rute

1 Samueli

2 Samueli

1 Mafumu

2 Mafumu

1 Mbiri

2 Mbiri

Ezara

Nehemiya

Estere

Yobu

Masalimo

Miyambo

Mlaliki

Nyimbo ya Solomo

Yesaya

Yeremiya

Maliro

Ezekieli

Danieli

Hoseya

Yoweri

Obadiya

Yona

Mika

Nahamu

Habakuku

Zefaniya

Hagai

Zekariya

Malaki

Chipangano cha Tsopano

Mateyu

Maliko

Luka

Yohane

Machitidwe a Atumwi

Aroma

1 Akorinto

2 Akorinto

Afilipi

Akolose

1 Atesalonika

2 Atesalonika

1 Timoteyo

2 Timoteyo

Tito

Ahebri

Yakobo

1 Petro

2 Petro

1 Yohane

2 Yohane

3 Yohane

Yuda

Chibvumbulutso

Tags:

Baibulo Mabukhu a Baibulo

🔥 Trending searches on Wiki Chichewa:

Mtsinje wa GangesEdgar LunguChengduCuritibaNelson MandelaPaltogaSchizophreniaZanco Mpundu MutemboMalimba MashekePongamia pinnataMliri wa kachilombo ka corona 2019-20EdirneComet C/2022 E3Yesu KristuMaryana IskanderMasewera a Olimpiki Ozizira a 2022Chifuwa ChachikuluJohannesburgXi JinpingMalawiFashion SakalaSandra MasonChilatiniSisay LemmaJudiciary waku MalawiNew York CityJaynagar MajilpurBaibuloNanjingLondonDhakaSu YungJack in the BoxMpiraChicagoMumbaiNorth AmericaMeyiMonica MusondaLolembaAdolf HitlerChiarabuEastern CapeAlbaniaISBNMpira ku ZambiaSanfourcheMao Zedong🡆 More