Lazarus Chakwera

Lazarus McCarthy Chakwera anabadwa pa 5 April 1955 ndipo ndi Malawi yemwe amadziwika bwino ndiza umbusa wa mulungu komanso ndale.

Iyeyu anakhalapo wankulu wa mpingo wa Assemblies of God of Malawi kwa zaka zopitilira 20, kufikira chaka cha 2013 pamene anayamba ndale ndipo wakhala president wa dziko la Malawi kuyambira nchaka cha 2020 mu mwezi wa June.

Lazarus Chakwera
Lazarus Chakwera

Tags:

Malawi

🔥 Trending searches on Wiki Chichewa:

AtombolomboVincent van GoghISBNSabata m'matchalitchi a tsiku lachisanu ndi chiwiriNorth AmericaBakili MuluziSomalilandNational Aeronautics and Space AdministrationNileZimbabwe African National UnionItalyWiki CommonsKamuzu BandaAlice Rowland MusukwaGame & WatchUnited StatesSouth AfricaСрбијаPulezidenti wa ZambiaNduna ya MalawiUfumu wa United KingdomHakainde HichilemaJohann Sebastian Bach (wolemba)Chikopa ya LithuaniaNchaloDonald TrumpKing Edward VIIIHalyna HutchinsPalestine2021 Kutuluka kwa FacebookDear Mama (B Flow song)Katemera wa matenda oumisa khosiUnited Arab EmiratesManchester United F.C.Bernard HaitinkOld TraffordMercedes-Benz W114Cape TownMacece,MachingaLolembaLily TemboDziko LapansiEast JerusalemBaibuloBanjulowks8🡆 More