Jimmy Donal Jimbo Wales (wobadwa pa August 7, 1966) ndi wazamalonda wa pa Intaneti wa ku America, wotchuka kwambiri monga wothandizira a Wikipedia ndi Wikia.
Wales anabadwira ku Huntsville, Alabama, United States. Kumeneko, anapita ku Randolph School. Kenaka adalandira madigiri a bachelor ndi a master pa ndalama. Mu 1996, iye ndi anzake awiri adayambitsa Bomis. Bomis inali malo ochezera pa intaneti ndi zosangalatsa komanso zokhudzana ndi anthu akuluakulu. Kampaniyo inapereka ndalama kwa Nupedia (2000-2003) ndipo pambuyo pake, Wiki Chichewa.
This article uses material from the Wikipedia Chichewa article Jimmy Wales, which is released under the Creative Commons Attribution-ShareAlike 3.0 license ("CC BY-SA 3.0"); additional terms may apply (view authors). Content is available under CC BY-SA 4.0 unless otherwise noted. Images, videos and audio are available under their respective licenses.
®Wikipedia is a registered trademark of the Wiki Foundation, Inc. Wiki Chichewa (DUHOCTRUNGQUOC.VN) is an independent company and has no affiliation with Wiki Foundation.