Zimbabwe

Zimbabwe ndi limodzi mwa maiko a kumwera kwa Afrika ndipo dzikoli ndi lomwe kale linkalamuliridwa muchisamunda cha angerezi pomwe akalitchula kuti Rhodesia.

Nsogoleri wadzikoli pakali pano ndi is VACANT amene anayamba kulamulira dzikoli pamene linalanda ulamuliro kuchokera kwa angerezi m'chaka cha 1980.

Zimbabwe

Potsatira zokambirana zothetsa mapokoso ndi chipolowe chomwe chinabuka pambuyo pamasankho apa 21 Marichi, 2008 a Morgan Tshangirai omwe ndi m'tsogoleri wa chipani cha Movement for Democratic Change anakhala Nduna yaikulu ya boma. New leader of Zimbabwe 24 November 2017 is Emmerson Mnangagwa.


Zimbabwe Zimbabwe

Tags:

AfrikaRhodesia

🔥 Trending searches on Wiki Chichewa:

Teresa TengUSMadagascar (firimu)Sandra MasonChingereziKubereka mwanaJacques OffenbachCzech RepublicNorthern CapeUnited KingdomEdgar LunguDemokilaseJapanSaint PetersburgAnthu a ChitumbukaZagrebBalakaChiarabuBaskin-RobbinsKatemera wa matenda oumisa khosiNlambalalaChifuwa chokoka mtimaLazarus ChakweraSurabayaBangkokUEFA Euro 2020Cape VerdeLeonardo da VinciBakili MuluziMzuzuKupha David AmessBaron Llewellin woyambaSchizophreniaMutinta HichilemaAsiaHalyna HutchinsNkhondo ya Russia-UkraineVietnamTriple HViennaDonald TrumpBarack ObamaDamascusBerlin2021 Kutuluka kwa FacebookVincent van GoghBrendan KennellyJoyce BandaBorneo🡆 More