Pa chingeleziconstitution Mumakhala malamuro akulu akulu adziko omwe amapereka mphanvu ku nthambi zosiyanasiyana za boma kapena anthu wamba, mabungwe osiyana siyana ndi ena ambiri omwe ali mu dziko kutsata malamulo amundzikomo.
Mwachitsanzo, mumakhala m'ndandanda wa m'ndondomeko zimene anthu ayenera kutsatira zomwe ndi ndi zofunika kudziko. Mumakhalanso maufulu a wanthu monga mdzika za dziko, uthenga okhudza mmene mthambi za boma ndi zomwe siziri za boma ziyenera ku gwilira ntchito, komanso uthenga okhudza mmene kusamvetsetsa kwa zo chitika za dziko kunga longosoleredwe.
This article uses material from the Wikipedia Chichewa article Malamulo olamulira dziko, which is released under the Creative Commons Attribution-ShareAlike 3.0 license ("CC BY-SA 3.0"); additional terms may apply (view authors). Content is available under CC BY-SA 4.0 unless otherwise noted. Images, videos and audio are available under their respective licenses.
®Wikipedia is a registered trademark of the Wiki Foundation, Inc. Wiki Chichewa (DUHOCTRUNGQUOC.VN) is an independent company and has no affiliation with Wiki Foundation.